15/06/2026
Malawi πππππππππ
Mdara wina adafika ndimwana pometa ndipo adamuwudza ometa uja kt awamete onse iwowo ndimwanayo ndipo adayamba m'bambo atamumalinza adayamba kumeta mwana uja alimkati bambo uja adamuwudza ometa k*ti akubwera kaye ndipo bambo uja adanyamuka mwana uja atamumalinza onse adakhala kumadikilira abambowo πππππ
After 3hrs
Ometq adadabwq munthu uja sak*tulukira ndipo adamufunsa mwana uja " kodi iwe bambo ako aja apita k*ti? Ndipo mwana adati " ineso sindikuwadziwa adangondinyamula amati tizamete ulere
Ometa:???????
ππππππππππ