30/12/2025
LIKE ZAMBIA LIKE MALAWI π²πΌ πΏπ²
Days ago Lusaka Chipata Road nseu unaduka moti anthu opita ku Malawi kuchoka ku Zambia adakanika kupitiliza ulendo.
Pano ku Kasungu Mseu wa M1 waduka mlatho wa Mpasadzi