Mbadwa Media

Mbadwa Media The home of latest news

Pa Biwi Triangle pachitika mistake pang'ono Van yafera pa nsewu.Mbadwa Media
12/07/2026

Pa Biwi Triangle pachitika mistake pang'ono Van yafera pa nsewu.

Mbadwa Media

Kampani ya Malavi Boxing Promotion yakonza nkhonya yovuta kwambiri pakati pa Yamikani Mtambo komaso Grey Chimkwapulo omw...
22/06/2026

Kampani ya Malavi Boxing Promotion yakonza nkhonya yovuta kwambiri pakati pa Yamikani Mtambo komaso Grey Chimkwapulo omwe akhale akulimbirana lamba wa National Lightweight pa 28 June ku Kamuzu Institute For Sports.

Patsikuli kukakhalaso nkhonya zina zapamwamba 6 zomwe zikakhale zikuthetheka.
Mbadwa Media

"Angadzaone Ngati Moyo Ndiophweka"M***a "The Boika" Mkwanda wati nthawi yakwana kuti Roy Yudah Afunde lona. "ndikumufuna...
29/04/2026

"Angadzaone Ngati Moyo Ndiophweka"

M***a "The Boika" Mkwanda wati nthawi yakwana kuti Roy Yudah Afunde lona. "ndikumufuna ndikamugonekeko pansi angawone ngati moyo ndiwophweka", Mkwanda wayankhula.

Awa ndi machine nokhaso mungathe kuona.

Source Malawi Boxing News

Esinati walakwa chani kuti mumkwenye chotete?, azibambo akhumudwa kuti Esinati wamenyedwa ndi atsikana osadziwika bwino ...
29/04/2026

Esinati walakwa chani kuti mumkwenye chotete?, azibambo akhumudwa kuti Esinati wamenyedwa ndi atsikana osadziwika bwino munsika waku Nselema.

Kampani yokonza nkhonya ya Malavi Boxing News Promotion yatsimikiza kuti pa 4 January, 2026 yakonza nkhonya zomwe zikach...
30/12/2025

Kampani yokonza nkhonya ya Malavi Boxing News Promotion yatsimikiza kuti pa 4 January, 2026 yakonza nkhonya zomwe zikachitikire Ku Kamuzu Institute for sports mu mzinda wa Lilongwe.

Nkhonya yaikulu iri pakati pa M***a Ajibu waku Malawi amene adzaswane ndi Simon Madanhire waku Zimbabwe, komaso nkhonya zina:
Byson Fuso Fighter Gwayani Vs Osgood Kayuni

Israel Money Machine Kam'mwamba Vs Yamikani Mtambo

Antony Banda Vs Alick Gogodo

Yusuf Ali Vs M***a Kananji

Robert Kachiza Vs Mike Phiri

Mbadwa Media

Address

0993412980
Lilongwe

Telephone

+265885567461

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mbadwa Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mbadwa Media:

Shortcuts

Share