Online bible study.

Online bible study. Mau a mulungu ndia ulele phuzilan kut moyo wanu wauzimu ukhale owala. Zomwe mulinazo phuzisan azanu kut aziwe.

Ngat muli ndi fuso lili lose lokhuza baibulo chonde tumizani uthenga SMS ku tigawane bib.

22/06/2026

πŸŒ™ Madalitso a Madzulo πŸŒ™

"Musataye mtima. Mulungu amene anakusungani lero adzakusunganinso mawa. Pumulani mwa mtendere, chifukwa Yehova akukusamalirani." πŸ™β€οΈ

πŸ“– "Usaope, chifukwa Ine ndili nawe." β€” Yesaya 41:10

22/06/2026

"Kwa Mulungu palibe chosatheka. Pitirizani kupemphera ndi kukhulupirira. πŸ™βœ¨ – Luka 1:37"

GOOD MORNING πŸŒ„

21/06/2026

"Ngakhale zinthu zitavuta bwanji, Mulungu ali ndi njira. Khulupirira Iye, pemphera, ndipo usataye mtima. πŸ™β€οΈ"

30/05/2026

Ogona Sadziwa
kanthu
Mulungu akhare
Maso ako usiku uno

Address

Kanengo
Lilongwe
KANENGO

Telephone

+265991893937

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Online bible study. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category