Yamikani macheza

Yamikani macheza Misesa. Soche

10/03/2023

Good morning everybody
😍😘😍😘 We have a Sweet friday God be with you each and everybody 🙏

29/12/2022

Uku kunali ku Mozambique pamene anthu anali ndi mwayi woti awonse chinsomba ichi. Chinsombachi , ndi chija chimatchedwa kuti : " whale 🐋"
Whale ndi nsomba yodziwika kwambiri ndipo imatalika kudutsa ma mita 11 Pena imafika mamita 12.65 ( 41.50 ft). Ndipo imalemera matani odutsa 21.5 ( 47, 000 lb ).
Ndi nsomba yaikulu, koma simadya anthu ndipo simavuladza anthu mwadala, ngati yawomba bwato , ndiye nkuti ndi ngozi chabe. Ndipo imakhala ndi moyo mpaka kudutsa zaka 80 zina zimafika zaka 90. Ngakhale izi zimatengera mtundu wa msombayi komano zambiri zimakhalitsa nkumangokulirakulirabe mpakatu zina zimadutsa ma mita 20 zikutalikiratalikirabe.

KOMA KODI KUNO KU MALAWI, CHINSOMBACHI, TINACHIPATSA KALE DZINA ?
pajatu kuno pafupipafupi chilichonse chili ndi dzina lakelake, ndiye amene akudziwako dzina la chinsomba ichi atiudzeko. Popedza mayiko ambiri amangochitchula kuti WHALE 🐋 basi.
Nanga kwathu kuno ? Osaiwala kupanga like page ili la lMfumu Solomo - Pabwalo tizionera limodzi zinthu zambiri.

05/12/2022

Mwaswera bwanji kulikonse komwe kuli makosana

28/11/2022

Uzifuna kulira ndy. Misozi isamatuluke ngat uliret .

Address

Kapeni Road
Blantyre
CHILLING

Telephone

+265880876870

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Yamikani macheza posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category