Mwayi Cee Photographer/Videographer

Mwayi Cee Photographer/Videographer Producer,music video, audio, photography and videographer basic in Lilongwe located at area 25.

26/08/2025

I can see Mwayi Cee Studio next year ikubweleranso iyiyi idzasiyana ndi yomwe inalipo kapena yomwe mwakhala mukuyiona kwa dzaka 15 dzapitazi.


1. And ulendo umenewo ma Artist 5 ajambulidwa ma video mwa ulele ndi dzapushanso ndekha nyimbo zawo.

2. Ma choir awiri a mwayi nawo adzajambulidwa ma video aulere.

Izi ndimachita kufuna kuthandiza maimbidwe kuti apite patsogolo ndati ziiii ndi cholinga zilipo ndikulongosola.

11/10/2023

Anthu kuno ku area 25 lilongwe Yepa village akukana kulandira ma 20 kwacha ndimati ndifunse kuti,boma lamvomereza zokana ndalama nanga kukana ndalama pomwe boma silinachotse ndalama imeneyo umakhala mulandu? Kwa anthu omwe mumadziwako kanthu tabwerani pano mutiunikireko.

    Yesterday work 23 May 2023
24/05/2023




Yesterday work 23 May 2023

  Location Area 25 B
09/05/2023




Location Area 25 B

Address

One
Lilongwe
8888223355

Telephone

+265991879283

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mwayi Cee Photographer/Videographer posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mwayi Cee Photographer/Videographer:

Share