M ZIRO MW

M ZIRO MW Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from M ZIRO MW, Photographer, Mangochi, Makanjila.

Tumiki wa Allah Muhammad ﷺ adat { akakhala kuti muthuyo ali  wazintchito zoyipa pamene geneza yanyamulidwa ndikuyikidwa ...
29/12/2025

Tumiki wa Allah Muhammad ﷺ adat { akakhala kuti muthuyo ali wazintchito zoyipa pamene geneza yanyamulidwa ndikuyikidwa paphewa wakufayo amati inu ine mozi mwayinu mukunditengela kuti ndipo mawu awawa amaveka kucholengedwa chilichose cha Allah kupatula muthu . .
{ Bukhar 1314}

Ndipo muthawi iyiyi ali muthu oti amachita zabwino sadandaula kathu ndipo amawonaso kuchedwa kukamusiya kumandako .

Ndisiku lamasawuso wallah kwa anthu ochulusa kucheza paduniya . Zipulumuseni nokha pachomwe chikuza.
Khalan ndizelu pozizindikila kuti umoyo ndili nawo ndiwokhala pang’ono .

Tizipepha Allah kuti imfa izatipeze tili ayiman ameen

Address

Mangochi
Makanjila

Telephone

+265888831826

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when M ZIRO MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category