Emm Nans Pictures

Emm Nans Pictures We offer graphics,, video and audio production

13/05/2026
10/05/2026

Kuvina kupose apa

Book your session today. 0886530884 / 0999051902
28/04/2025

Book your session today.
0886530884 / 0999051902

02/04/2025

Mzako watuluka momo nthiti zonse zikuonekera,iwe mkuzalowanso momo.Ukatuluka dzotupa kumaliseche uziti "akwathu amandisaka".๐Ÿšถ๐Ÿฅฑ

28/09/2022

TILI MMOYO OSAUSA KWAMBIRI.
Pomwe amalawi akulira mosalekeza pankhani yakukwera kwa katundu nziko muno. Highlight creation media yapexa nkhan ina yokhuza kwambiri. Zaululika k*ti sukulu zonse za nziko muno za boma maka za primary zikhala zikuyamba kulandira ndalama kapena k*ti sukuku fees yokwana kwa mwana aliyense K10 000 MW.
Izi ndizo zizindikiro zakusonyeza k*ti zaka zikubwerazi malawi azakhala ndi anthu ambiri osaphunzira.
Koma funso mkumati kodi ncifukwa cani bola lacita ciganizoci colinga chawo ndicaniโ“
Katundu ndiuyu wakwerayi tikugona nd njala kholowa alipo koma UFA mulibemo kodi zitheka kumagonabe nd njala colinga mwana aphunzire kumapeto ake ncito izizasowansoโ“
Dzko likukomera anthu olemera kale nanga izi ndicani ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ timalephera kupereka yeni yeniyi K500 yachitukuko nanga K10 000 titenga k*tiโ“
Amalawi anzanga ziwani k*ti dziko la Malawi ndilimodzi mwa maiko omwe samalemekeza maphunziro ,, limbikani ncito zamaja mumacizo poti sukulu ikunka ikuvuta vuta.
Izi nd zocepa zomwe zapexeka kanthawi ino.
Pangani like k*ti nkhan zisakuphonyeni pa page inoyi.
Malawi wankaka ndi uci uja wasanduka ovuda.I๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

24/09/2022

Akazi opita kusikelo wa pasi MULIBWANJI ?
chosecho ku lodge mudaapit pa njale๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‰

10/09/2022

Zoti muli pa chikond tikuziwa koma zoti mulibe ndalama abea anuo akuziwaโ“
๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜ญ๐Ÿ‘†๐Ÿ™

10/09/2022

RIP Queen Elizabeth.
๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

06/08/2022

KUPOIRA KWA AKAZI.

Bengo___ martha zabwino?

Martha ___ bhobhotu.

Bengo ___ ok pali nkhan yot tinvane,zitheka?

Martha ___ bola zikhale zanzeru.

Bengo ___ ukudziwa, ineyo ndi munthu iwenso ndi munthu ndie zofooka za ine ungakwanitse ndi iweyo china chake chandiuza choncho.

Martha ___ tangonenani nkhani osazembera china chake apa.

Bengo ___ ndakhala ndikusaka wachikondi ndipo mtima wanga wandiuza k*ti iweyo nde weniweni ndpo ndatsimikizad k*ti nditha kukukwatira.

Martha ___ inutu ndinu achitsilu,ine ai ndipo ndingapange chibwenzi ndi iwe? Kubeetsaaa chaani?

Bengo ___ tanvera chikondi sichitengera k*t uyu ndi otani kaya amatani chimapanga zomwe ichocho chikuziwa ndipo ndikukulonjeza k*ti ndizakhala okhulupirika kwa iwe mu nyengo zonse.

Martha ___ kkkkkk koma zinazi ine ai ndithu.bengo pita kwa wina ineyo si level yako ndipo uli k*tali.

Bengo ___ sinthawi yonyozana ino ngati zili choncho aaa its okay basi zatha koma zikomo pondipatsa nthawi yolankhulana nawe bye.

Martha ___ mmmmm ponda bho ena akuone.

Bengo atanyamuka anakumana ndi mzake wapantima wa martha yemwe ndi Eliza.bengo atamuona eliza mutu wake unabalalika coz eliza anali ngenge.

Bengo ___ aunt! Tingalankhulaneko 2min?

Eliza ___ aaa ndili pachangu!

Bengo ___ ndi nkhani yochepa koma itha kukula ndi mmene mungandiyankhile.

Eliza ___ okay m***a kulankhula.

Bengo ___ choyamba dzina lanu ndindan?

Eliza ___ ndine Eliza.

Bengo___ ine ndi bengo aunt ndsaname ndpo ndsakuchedwetseni kukuonani ndakuonani apa mtima wanga wakanika.

Eliza ___ muk*tanthauza chan?

Bengo ___ ngat uli pabanja ndikusiya k*ti upite koma ngati usali pa banja ineyo ndakonzeka kukhala wako ok*thandizira pa zosowa zako.

Eliza ___ mmmm achimwene tamasulani bwinobwino.

Bengo ___ ndakukondani k*ti mukhale mkazi wanga.

Eliza___ ok poti ndili pa changu tengani tikambrana nthawi ina.

Bengo ___ zikomo kwambiri ndikuimbirani.

Eliza ___ ok chabwino.

Patapita masiku awiri bengo anaimba 4n ndipo ananvana moti analola.

Martha

Address

Mulanje
HL

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Emm Nans Pictures posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category