UNCLE KHIRI

UNCLE KHIRI if you are looking for high quality video and photos you have reached the right place

Bambo ali makwasa kubwelera kwawo atalandila thandizo la transport.    kuwapatsa Mr alli Makwasa transport kuti azipita ...
05/06/2025

Bambo ali makwasa kubwelera kwawo atalandila thandizo la transport. kuwapatsa Mr alli Makwasa transport kuti azipita kumudzi, atakhala ntown kwa ma week tsopano kupemphesa mcholinga choti apeze transport yobwerera kwao ku balaka, bambowa ali ndi vuto la stroke, ndipo analumala mbali imodzi, chomcho amazapanga physiotherapy ku zomba hospital, koma transport imawavuta kupeza chomcho amavutika kubwelera kumudzi https://youtu.be/XsLdJuWN8yc

Thandizo la zovala zakale, chakudya, soap kaya ndalama zonsezo muthandiza. 0881768837
15/05/2025

Thandizo la zovala zakale, chakudya, soap kaya ndalama zonsezo muthandiza. 0881768837

Iyi ndi nkhani ya mayi Magret Chimwaza omwe amachokera mu mzinda wa zomba. mayiwa ali ndi zaka 77. ndipo kamba kamavuto ...
05/04/2025

Iyi ndi nkhani ya mayi Magret Chimwaza omwe amachokera mu mzinda wa zomba. mayiwa ali ndi zaka 77. ndipo kamba kamavuto azachuma amapemphesa ntauniyi. amasaka ntchito koma anthu amawakana kuti ndi achikulire sangakwanitse kugwila ntchito iliyonse. onera kufotokoza za momwe anayambira kupemphesa. also follow UNCLE KHIRI for more updates. watch the video here

Iyi ndi nkhani ya mayi Magret Chimwaza omwe amapemphesa Ntownship ya zomba, mayiwa ndi achikulire ndipo ali ndi zaka 77, mayiwa amakanidwa ntchito chifukwa c...

24/03/2025

Dzina la bambo amenewa ndi Harry.
A harry amapempha town ya Zomba Chifukwa Cha vuto la ulumali wa miyendo, koma ali ndikuthekera kopanga ntchito zamanja ngati kukhoma mapoto komaso kuluka mphasa chabe mpamba wawo unagwa kamba kakukwera kwazinthu nde anaganiza zongoyamba kupempha ngakhale sikhumbo lawo.
Kuti mulumikizane nawo imbani kapena tumizani uthenga pa whatsapp ku number iyi 0881768837 Christopher trapence

Lets bring together positivity towards people with disabilities and who beg
24/03/2025

Lets bring together positivity towards people with disabilities and who beg

05/10/2024

Thanks to those who have started sending help/money for Mrs and Mr kanasoni for more details this is thr link:

Tiyeni tithandize mayi Aida Kanasoni ndi Banja LawoMai Aida Kanasoni ndi amuna awo akuvutika kwambiri kamba ka vuto la u...
04/10/2024

Tiyeni tithandize mayi Aida Kanasoni ndi Banja Lawo

Mai Aida Kanasoni ndi amuna awo akuvutika kwambiri kamba ka vuto la ulumali zikuwavuta kwambiri kuti apeze chakudya, komaso chisamaliro cha umoyo wabwino
chithandizo china chilichonse chithandiza kusintha zinthu, Ndalama,chakudya, Mapemphero ndi zina zonse.

Zikomo kwambiri pakuzipereka pa support iliyonse yofuna kuthandiza banjali
Omwe akufuna kusonkha, tikugwiritsa ntchito:
Mpamba: Airtel money:
+265897777394 +265990855301

standard bank account: 9100005662475
Christopher Trapence city center Branch Lilongwe

Target yathu ndi K250,000, zomwe zikagwiritsidwe, powagulira Chakudya ndi zosowa zina.
Limodzi tikhonza kukwanitsa kusintha nyengo zawo, zikomo.

Address

Chinamwali
Zomba
265881768837

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when UNCLE KHIRI posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share