Pluto Studios II

Pluto Studios II Photography | Videography | Framing

05/06/2026

Dzana tinapanga ka post koti timwaza ma Data Bundle kwa amwayi. Lero tagawa. Tiwunikiraneko ziwiri zitatu za moyo wu, zomwe tawona kudzera mu ka nkhani ka ma bundle komweka:

1. The instruction was "Comment with your phone number and tag three friends". Ena they really wanted the bundle but failed this very simple instruction. Some just put their number there and hoped for the best.
Lesson: Even luck requires effort. You can never win a Billion Kwacha lottery if you don't buy even a single ticket. Sikadza kokha. Tsiku lina muzasephana ndi Batala wa ku Max & Sherry.

2. Some tagged the three friends. Enanso kudutsa, koma osaika number yawo.
Lesson: You can't achieve anything in life if you don't satisfy the minimum requirements. Kumafatsa with instructions in everything; exams, interviews, work etc. Tsono ifeyo bundle yo tiponya kuti?

3. Ena akuti "Ambuye ichi chokha chisandipitilire😭". Just like that... No tagging friends, no phone number...
Lesson: Tisamamuyese Mulungu.

Bottom line: Zambiri zopindulitsa mmoyo wu zimatiphonya chifukwa sitikhala serious. The good thing is we all have room to improve and be better. The lessons shared are not about data bundles, they are about life in general.

Kaya malangizo amveka?

📸

The 10 ChezaFaya Bundles that PLUTO promised dzana have been fulfilled!Congratulations 🎊 to the 10 lucky winners who par...
05/06/2026

The 10 ChezaFaya Bundles that PLUTO promised dzana have been fulfilled!
Congratulations 🎊 to the 10 lucky winners who participated!!!
Nanga Molalo akhale wanu, bundle nso wanu?

Kwa anthu ena ka bundle akaka si nkhani, koma kwa ena, akaka katha kuwasuntha. We want 10 lucky people to benefit from t...
03/06/2026

Kwa anthu ena ka bundle akaka si nkhani, koma kwa ena, akaka katha kuwasuntha. We want 10 lucky people to benefit from this by tonight.

Drop your number and tag at least 3 friends to join the fun that happens on our page.

Nanga Morale akhale wanu, bundle yo user nso wanu?
📸

Couples who laugh together😍❤️😍Inuyo mukadzakumana ndi that one person who was made just for you, sizizasowa.
02/06/2026

Couples who laugh together😍❤️😍
Inuyo mukadzakumana ndi that one person who was made just for you, sizizasowa.

A big sign of self love is you carrying your beautiful self to the studio for some fire photos for no good reason... jus...
02/06/2026

A big sign of self love is you carrying your beautiful self to the studio for some fire photos for no good reason... just loads of self love.
📸: Glory 🔥

Kwa afoto ajawa munanena kuti simudzapitakonso zitavuta zitatani, chifukwa cha?
01/06/2026

Kwa afoto ajawa munanena kuti simudzapitakonso zitavuta zitatani, chifukwa cha?

The beautiful Memoe Memoree Phree was born today! Happy birthday Memory! 🎂
01/06/2026

The beautiful Memoe Memoree Phree was born today! Happy birthday Memory! 🎂

Kodi ndekuti ukuku kukakhala ngogole 🍕 tidziopa kukakomentako? 🙆‍♂️ Ife nde tidukaa... tidukaaa😭  📸
01/06/2026

Kodi ndekuti ukuku kukakhala ngogole 🍕 tidziopa kukakomentako? 🙆‍♂️ Ife nde tidukaa... tidukaaa😭 📸

Kodi aise Partner Pluto Studios II takuputa?

Kodi anthu anakupanga tag dzulo aja unawagulira Pizza ija?

Ukuona ngati aiwala? Ugulatu iweyo!

31/05/2026

Koma tikuyamba ubale ndi awawa, aliyense ankangoti "Welokhamu Patenala🥰", popandako otiuza chilungamo kuti "Vala Zilimbe mphwanga ndi ka camera kakoko, uziona.."🤦🏾

Achina Kadazi ku Max & Sherry ndi tianthu take tija kufuna kutamika ati 🙄
31/05/2026

Achina Kadazi ku Max & Sherry ndi tianthu take tija kufuna kutamika ati 🙄

Address

Zomba

Opening Hours

Monday 08:00 - 18:00
Tuesday 08:00 - 17:30
Wednesday 08:00 - 17:30
Thursday 08:00 - 17:30
Friday 08:00 - 17:30
Saturday 08:00 - 17:00
Sunday 10:00 - 16:00

Telephone

+265999158663

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pluto Studios II posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Pluto Studios II:

Share