Nyasa Narrative stories

Nyasa Narrative stories The lovely God love us Teaching and learning to next generation

11/04/2023
30/11/2020

MASAZI
awa ndimatenda womwe amayamba pazifukwa zosiyana siyana
Ambiri amakhulupilira kuti ndimatenda womwe amayamba kamba kazakudya zomwe zili ndi spicy wambiri ngati Volse Soyo pieces ndizina zambiri koma aza umoyo amati pomwe tikuganiza kwambiri tingathe kudwala matendawa .
Kodi ndizoganiza ziti zomwe zingatipangitse kudwala matendawa
Mavuto womwe timakumana nawo monga kusowa kwa fees makolo amayamba kuganiza mopitilira muyizo.
Muli ku school azunu ena akudya zinthu zabwino inu mulibe pocket money mukalingalira kwambiri kuti why ine mungathe kudwalanso matendawa.

KODI MUNTHU AMACHIRA
answer ndi yes
Amachira ndipo sangadzadwalenso.
Tiyeni tiona makhwala ake komanso ndimene tingapewere.

1.Tengani Mthochi(fresh banana) itatu yoti siyinapse (green)
2.isendeni kapena kuti muichotse chakunja chakacho ndimpeni or manja.
3.dulani ma piece ma piece woti sangavute kuuma.
4.yanikani pa dzuwa ndipo aume ngati muja tichitira ufa.
5.ngati auma tengani ma piece ndikusakaniza ndi mchere pang'ono ndikuyamba kusinja mumtondo ngati palibe mtondo mungathe kupere ndi chili chonse chomwe tikufuna kupanga ndi ufa basi.
Ndikudziwa njira ndizambiri zopangira ufa mungathe kusefa ngati chosefera chilipo ngati palibe onetsetsani kuti wapeleka.
6.phikani phara ndipo musathiremo mchere ndikuthiramo soupen imodzi ndikutakasa kuti sisakanikirane bwino pangani izi mawa ndi madzulo kwamasiku 15 days.ngati simukuona kusintha kuli konse kaonaneni ndi Doctor.

Pewani kuganiza kwambiri.

Whatsapp number+27738816720
Jaiman GB Mkomakumbuyo
[email protected]

21/10/2020

True relationships are not formed out of any materialistic expectations but to exchange love and care. When people connect with others for wealth, power or influence, it is only to satisfy their own greed.

When a relationships loses it’s basic virtue of being truthful, that relation doesn’t last long and only ends up in misery. The relations based on self motives will always break you. The true bonds in life are the bonds of soul. There is a purpose but the purpose is to together find the meaning of life.

Never let financial gain be the reason to develop a friendship or a close relationship. Wealth can be created but you won’t be able to create your broken self again.

Dr Bhawna Gautam

What can we learn from this picture* not all opportunities are to be taken some are traps* a person can become so determ...
10/10/2020

What can we learn from this picture

* not all opportunities are to be taken some are traps
* a person can become so determined and destroy another person that they become blind and end up destroying themselves.
*You fight best in your natural element and environment the bird has an advantage in the has natural element.
* know your limits we all have them.
* sometimes the best response to provocation is not to fight.
* sometimes to accomplish something you need team to work you will not always win alone
🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁

26/09/2020

Hi Malawi
Hi Africa
🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁🍁

01/09/2020

That's life

KUSELI KWA MAWA KULINJI part 1Zikomo amfumu abokosi potilandira mudzi wanu uno choyamba tithokozenso anthu amdera lino p...
16/08/2020

KUSELI KWA MAWA KULINJI

part 1

Zikomo amfumu abokosi potilandira mudzi wanu uno choyamba tithokozenso anthu amdera lino pobwera pamkumano uno mutava kuyitana muzambiri zomwe tabwera kuti tidzakudziwitseni monga mukudziwa masabata akubwerawa kuli masankho wosankha amtsogoleri anamdera anatero mulangizi yemwe anabwera mdera lineri

Sonkhano utatha tonse tinabwelera makwathu

13/08/2020

Like my page

hΓ­ mΞ±lΞ±wΓ­
14/06/2020

hΓ­ mΞ±lΞ±wΓ­

Address

Paarl

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyasa Narrative stories posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Nyasa Narrative stories:

Share

Category